YONI DETOX PEARLS
Description
YONI DETOX PEARLS Pack of 3 pearls@K10,500 only °Amachotsa za white zomwe zimathimbilitsa pant or kuchotsa fungo lonukha Ku ndata. °Yoni pearls akakhala Ku ndata amachotsa mauka, kuchiza kuyabwa yabwa, kuchotsa ma bacteria,matuza, zilonda, njerewere. °Yoni pearls amabweza Ku ndata ,Kwa masiku ochepa basi or tsiku lomwelo. °Amachiza zotupa za mchiberekero, cyst, °Yoni pearls amachiza zizindikilo za cancer kupweteka ya khomo la mchiberekero. °Yoni pearls amachiza komanso kutsegula fallopian tube omwe anatsekeka °Yoni pearls amapereka zinc yemwe amabweretsa ubereki,ukazi obereka. °Yoni pearls amabweretsa chilakolako, nyesi Kwa Mkazi. °Yoni pearls amachotsa toxic yemwe amapangitsa kuti mkazi azipita padera. °Amaonjezera ma hormones komanso kukhwimitsa chiberekero chikhale cholandila unborn baby
Questions About This Product?
Our skincare experts are here to help you make the right choice
Chat with Expert